National anthem of Malawi: Mlungu dalitsani Malaŵi

The Malawian national anthem was written by Michael-Fredrick Paul Sauka and composed by Michael-Fredrick Paul Sauka.

Mlungu dalitsani Malaŵi, Mumsunge m'mtendere. Gonjetsani adani onse, Njala, nthenda, nsanje. Lunzitsani mitima yathu, Kuti tisaope. Mdalitse Mtsogoleri nafe, Ndi Mayi Malaŵi. Malaŵi ndziko lokongola, La chonde ndi ufulu, Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri, Ndithudi tadala. Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu, N'mphatso zaulere. Nkhalango, madambo abwino. Ngwokoma Malaŵi. O Ufulu tigwirizane, Kukweza Malaŵi. Ndi chikondi, khama, kumvera, Timutumikire. Pa nkhondo nkana pa mtendere, Cholinga n'chimodzi. Mayi, bambo, tidzipereke, Pokweza Malaŵi.

Malawi National symbols

⏪ Back to the national symbols of Malawi

What is Malawi known for?

Malawi is known for its friendly people, freshwater lakes, and the famous Lake Malawi which is one of the deepest lakes in the world

Where is Malawi located?

Neighbours of Malawi

Questions & Answers about Malawi

Compare Malawi with other countries

with

Compare Malawi with its neighbours

Guess the Flags Quiz